Yesaya 49:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Yehova akunena kuti: “Ngakhale anthu amene agwidwa ndi munthu wamphamvu adzalandidwa,+Ndipo amene anagwidwa ndi wolamulira wankhanza adzapulumutsidwa.+ Ndidzalimbana ndi aliyense amene akulimbana nawe,+Ndipo ana ako ndidzawapulumutsa.
25 Koma Yehova akunena kuti: “Ngakhale anthu amene agwidwa ndi munthu wamphamvu adzalandidwa,+Ndipo amene anagwidwa ndi wolamulira wankhanza adzapulumutsidwa.+ Ndidzalimbana ndi aliyense amene akulimbana nawe,+Ndipo ana ako ndidzawapulumutsa.