Yesaya 58:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova azidzakutsogolerani nthawi zonseNdipo adzakupatsani zinthu zofunika ngakhale mʼdziko louma.+Iye adzalimbitsa mafupa anuNdipo inu mudzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino,+Ndiponso ngati kasupe amene madzi ake saphwera.
11 Yehova azidzakutsogolerani nthawi zonseNdipo adzakupatsani zinthu zofunika ngakhale mʼdziko louma.+Iye adzalimbitsa mafupa anuNdipo inu mudzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino,+Ndiponso ngati kasupe amene madzi ake saphwera.