Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 16:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Komanso Samariya+ sanachite machimo ofika ngakhale hafu ya machimo ako. Koma iwe unapitiriza kuchulukitsa zinthu zonyansa zimene unkachita kuposa abale ako, moti unachititsa kuti azichemwali ako aoneke ngati olungama chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene unkachita.+

  • Ezekieli 23:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Wamkulu dzina lake anali Ohola,* wamngʼono anali Oholiba.* Akazi amenewa anakhala anga ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi. Ohola akuimira Samariya+ ndipo Oholiba akuimira Yerusalemu.

  • Ezekieli 23:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mchemwali wake Oholiba ataona zimenezi, chilakolako chake chinafika poipa kwambiri ndipo uhule wake unafika poipa kuposa wa mkulu wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena