Yeremiya 44:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ine ndine wokonzeka kuwabweretsera tsoka, osati zinthu zabwino.+ Anthu onse a ku Yuda amene ali mʼdziko la Iguputo adzafa ndi lupanga ndiponso njala mpaka atatheratu.+ Yeremiya 45:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Umuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Taona! Zimene ndamanga ndikuzigwetsa ndipo zimene ndadzala ndikuzizula. Ndichita zimenezi mʼdziko lonse.+
27 Ine ndine wokonzeka kuwabweretsera tsoka, osati zinthu zabwino.+ Anthu onse a ku Yuda amene ali mʼdziko la Iguputo adzafa ndi lupanga ndiponso njala mpaka atatheratu.+
4 Umuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Taona! Zimene ndamanga ndikuzigwetsa ndipo zimene ndadzala ndikuzizula. Ndichita zimenezi mʼdziko lonse.+