2 Mafumu 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri ndi alonda atatu apakhomo.+ 2 Mafumu 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo ku Ribila mʼdziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anatengedwa kudziko lawo nʼkupita nawo ku ukapolo.+
18 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri ndi alonda atatu apakhomo.+
21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo ku Ribila mʼdziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anatengedwa kudziko lawo nʼkupita nawo ku ukapolo.+