Yeremiya 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Mfumu ya Yuda imene yakutumani kudzafunsira kwa ine mukaiuze kuti: “Taonani! Asilikali a Farao amene akubwera kudzakuthandizani adzabwerera kwawo ku Iguputo.+ Ezekieli 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho anthu onse amene akukhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,Chifukwa sanalinso ngati ndodo yothandiza nyumba ya Isiraeli poyenda, koma anali ngati tsekera.*+
7 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Mfumu ya Yuda imene yakutumani kudzafunsira kwa ine mukaiuze kuti: “Taonani! Asilikali a Farao amene akubwera kudzakuthandizani adzabwerera kwawo ku Iguputo.+
6 Choncho anthu onse amene akukhala ku Iguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,Chifukwa sanalinso ngati ndodo yothandiza nyumba ya Isiraeli poyenda, koma anali ngati tsekera.*+