-
Danieli 10:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 ndinaona munthu atavala nsalu+ ndipo mʼchiuno mwake anali atamangamo lamba wa golide wa ku Ufazi. 6 Thupi lake linkanyezimira ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inkawala ngati mphezi, maso ake ankaoneka ngati miyuni yamoto, manja ake komanso mapazi ake ankaoneka ngati kopa*+ wonyezimira, ndipo mawu ake ankamveka ngati mawu a gulu lalikulu la anthu.
-