Ezekieli 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Iwe mwana wa munthu, losera zoipa zimene zidzachitikire Gogi+ ndipo umuuze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndikupatsa chilango iwe Gogi, mtsogoleri wamkulu* wa Meseki ndi Tubala.+
39 “Iwe mwana wa munthu, losera zoipa zimene zidzachitikire Gogi+ ndipo umuuze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndikupatsa chilango iwe Gogi, mtsogoleri wamkulu* wa Meseki ndi Tubala.+