1 Mbiri 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Hamu anali Kusi,+ Miziraimu, Puti ndi Kanani.+