Ezekieli 39:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzakubweza nʼkukutsogolera kuti uchoke kumadera akutali kwambiri akumpoto+ ndipo ndidzakubweretsa kumapiri a ku Isiraeli.
2 Ndidzakubweza nʼkukutsogolera kuti uchoke kumadera akutali kwambiri akumpoto+ ndipo ndidzakubweretsa kumapiri a ku Isiraeli.