Yeremiya 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: ‘Mʼdziko labwinja lino, lopanda anthu kapena ziweto komanso mʼmizinda yake yonse, mudzakhalanso malo odyetserako ziweto kumene abusa azidzapumitsirako ziweto zawo.’+
12 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: ‘Mʼdziko labwinja lino, lopanda anthu kapena ziweto komanso mʼmizinda yake yonse, mudzakhalanso malo odyetserako ziweto kumene abusa azidzapumitsirako ziweto zawo.’+