Ezekieli 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu a ku Dedani+ ankachita nawe malonda. Iwe unalemba ntchito anthu oti azikuchitira malonda mʼzilumba zambiri. Anthuwo ankakupatsa minyanga+ komanso mitengo ya phingo ngati mphatso.*
15 Anthu a ku Dedani+ ankachita nawe malonda. Iwe unalemba ntchito anthu oti azikuchitira malonda mʼzilumba zambiri. Anthuwo ankakupatsa minyanga+ komanso mitengo ya phingo ngati mphatso.*