-
Ezekieli 38:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Pakapita masiku ambiri, iwe udzaitanidwa. Ndiye pakadzapita zaka zambiri, udzalowa mʼdziko la anthu amene anabwerera kwawo. Anthu amenewa anapulumuka, lupanga litawononga dziko lawo. Kenako anasonkhanitsidwa pamodzi kuchokera kumitundu ina ya anthu nʼkukakhala kumapiri a ku Isiraeli amene anakhala ali owonongeka kwa nthawi yaitali. Anthu amene akukhala mʼdzikoli anawabwezeretsa kwawo kuchokera kwa anthu a mitundu ina. Onsewo akukhala mʼdzikoli motetezeka.+
-