Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoweli 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yehova adzabangula kuchokera ku Ziyoni,

      Ndipo adzalankhula mokweza ali ku Yerusalemu.

      Kumwamba ndi dziko lapansi zidzagwedezeka.

      Koma Yehova adzakhala malo othawirako a anthu ake,+

      Malo achitetezo champhamvu kwa Aisiraeli.

  • Nahumu 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.

      Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi wokonzeka kusonyeza mkwiyo wake.+

      Yehova amabwezera adani ake,

      Ndipo adani ake amawasungira mkwiyo.

  • Zekariya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Atapatsidwa ulemerero, Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene ankakulandani zinthu zanu,+ chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani, akukhudza mwana wa diso langa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena