Zekariya 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mliri umene Yehova adzagwetsere anthu onse a mitundu ina amene amamenyana ndi Yerusalemu+ ndi uwu: Munthu aliyense mnofu wake udzawola ali chiimire, maso ake adzawola ali mʼmalo mwake ndiponso lilime lake lidzawola mʼkamwa mwake.
12 Mliri umene Yehova adzagwetsere anthu onse a mitundu ina amene amamenyana ndi Yerusalemu+ ndi uwu: Munthu aliyense mnofu wake udzawola ali chiimire, maso ake adzawola ali mʼmalo mwake ndiponso lilime lake lidzawola mʼkamwa mwake.