Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 9:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako nʼkuloza kumwamba kuti matalala agwe mʼdziko lonse la Iguputo,+ kuti agwere anthu, nyama ndi zomera zonse mʼdziko la Iguputo.”+

  • Yoswa 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atafika pamalo otsetsereka otchedwa Beti-horoni pothawa Aisiraeli, Yehova anayamba kuwagwetsera matalala akuluakulu mpaka kukafika ku Azeka ndipo adaniwo ankafa. Amene anaphedwa ndi matalalawo anali ambiri kuposa amene Aisiraeli anawapha ndi lupanga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena