2 Samueli 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zikatero, ngakhale mwamuna wolimba mtima ngati mkango+ adzachita mantha kwambiri. Chifukwa Aisiraeli onse akudziwa kuti bambo anu ndi munthu wamphamvu+ ndipo amuna amene ali nawo ndi olimba mtima. Miyambo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,Koma olungama amakhala olimba mtima ngati mkango.*+
10 Zikatero, ngakhale mwamuna wolimba mtima ngati mkango+ adzachita mantha kwambiri. Chifukwa Aisiraeli onse akudziwa kuti bambo anu ndi munthu wamphamvu+ ndipo amuna amene ali nawo ndi olimba mtima.