-
Ezekieli 42:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Pafupi ndi malo opanda kanthu komanso nyumba imene inali kumadzulo, mkati* mwa mpanda wamiyala wa bwalo, kumbali yakumʼmawa, kunalinso nyumba zodyera.+ 11 Pakati pa nyumba zodyerazo panali njira yofanana ndi ya nyumba zodyera za mbali yakumpoto.+ Mulitali ndi mulifupi mwa nyumbazo, makomo otulukira komanso kamangidwe kake zinali zofanana ndi za nyumba za kumpoto zija. Makomo ake olowera
-