-
Ezekieli 1:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Yehova analankhula ndi Ezekieli,* mwana wa wansembe Buzi, pamene anali mʼdziko la Akasidi+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara. Kumeneko mphamvu za Yehova zinayamba kugwira ntchito pa iye.*+
4 Ndinaona mphepo yamkuntho+ ikuchokera kumpoto. Ndinaonanso mtambo waukulu komanso moto walawilawi*+ utazunguliridwa ndi kuwala. Pakati pa motowo panali chinachake chooneka ngati siliva wosakanikirana ndi golide.+
-