Ezekieli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamene ndinkaona masomphenyawo, ndinaona kuti pamwamba pa thambo limene linali pamwamba pa mitu ya akerubi, panali chinachake chooneka ngati mwala wa safiro. Chinthucho chinkaoneka ngati mpando wachifumu.+
10 Pamene ndinkaona masomphenyawo, ndinaona kuti pamwamba pa thambo limene linali pamwamba pa mitu ya akerubi, panali chinachake chooneka ngati mwala wa safiro. Chinthucho chinkaoneka ngati mpando wachifumu.+