Ekisodo 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo anaona Mulungu wa Isiraeli.+ Pansi pa mapazi ake pankaoneka ngati miyala ya safiro yoyalidwa bwino, yoyera ngati kumwamba.+ Salimo 96:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene amakhala pali ulemu ndi ulemerero.+Mphamvu ndi kukongola zili mʼnyumba yake yopatulika.+ Ezekieli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamene ndinkaona masomphenyawo, ndinaona kuti pamwamba pa thambo limene linali pamwamba pa mitu ya akerubi, panali chinachake chooneka ngati mwala wa safiro. Chinthucho chinkaoneka ngati mpando wachifumu.+
10 ndipo anaona Mulungu wa Isiraeli.+ Pansi pa mapazi ake pankaoneka ngati miyala ya safiro yoyalidwa bwino, yoyera ngati kumwamba.+
10 Pamene ndinkaona masomphenyawo, ndinaona kuti pamwamba pa thambo limene linali pamwamba pa mitu ya akerubi, panali chinachake chooneka ngati mwala wa safiro. Chinthucho chinkaoneka ngati mpando wachifumu.+