1 Mafumu 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+ Salimo 99:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 99 Yehova wakhala Mfumu.+ Mitundu ya anthu injenjemere. Iye wakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi.+ Dziko lapansi ligwedezeke. Yesaya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova atakhala pampando wachifumu wolemekezeka komanso wokwezeka,+ ndipo zovala zake zinadzaza mʼkachisi. Chivumbulutso 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako nthawi yomweyo mzimu wa Mulungu unayamba kugwira ntchito mwa ine ndipo mpando wachifumu unaoneka uli pamalo ake kumwamba, wina atakhalapo.+
19 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+
99 Yehova wakhala Mfumu.+ Mitundu ya anthu injenjemere. Iye wakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi.+ Dziko lapansi ligwedezeke.
6 Chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova atakhala pampando wachifumu wolemekezeka komanso wokwezeka,+ ndipo zovala zake zinadzaza mʼkachisi.
2 Kenako nthawi yomweyo mzimu wa Mulungu unayamba kugwira ntchito mwa ine ndipo mpando wachifumu unaoneka uli pamalo ake kumwamba, wina atakhalapo.+