Ezekieli 36:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzakupatsani mtima watsopano+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa inu.+ Ndidzachotsa mtima wamwala+ mʼmatupi anu nʼkukupatsani mtima wamnofu.*
26 Ndidzakupatsani mtima watsopano+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa inu.+ Ndidzachotsa mtima wamwala+ mʼmatupi anu nʼkukupatsani mtima wamnofu.*