Salimo 106:37, 38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ankapereka nsembe ana awo aamunaKomanso ana awo aakazi kwa ziwanda.+ 38 Ankakhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna komanso a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.
37 Ankapereka nsembe ana awo aamunaKomanso ana awo aakazi kwa ziwanda.+ 38 Ankakhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna komanso a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.