Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 21:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Iwe mwana wa munthu, losera kuti, ‘Izi nʼzimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena zokhudza mbadwa za Amoni ndi mawu awo onyoza.’ Unene kuti, ‘Lupanga! Lupanga lasololedwa kuti liphe anthu. Lapukutidwa kuti liwononge komanso kuti liwale ngati mphezi.

  • Ezekieli 21:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mudzakhala ngati nkhuni pamoto.+ Magazi anu adzakhetsedwa mʼdzikolo ndipo simudzakumbukiridwanso, chifukwa ine Yehova ndanena.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena