Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamwamba pake panali aserafi. Mserafi aliyense anali ndi mapiko 6. Aliyense anaphimba nkhope yake ndi mapiko awiri, anaphimba mapazi ake ndi mapiko awiri ndipo mapiko ena awiriwo ankaulukira.

  • Ezekieli 10:20, 21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Amenewa anali angelo amene ndinawaona pansi pa mpando wachifumu wa Mulungu wa Isiraeli kumtsinje wa Kebara,+ choncho ndinadziwa kuti anali akerubi. 21 Angelo onse 4 anali ndi nkhope 4 komanso mapiko 4. Ndipo pansi pa mapiko awo panali chinachake chooneka ngati manja a munthu.+

  • Chivumbulutso 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Aliyense wa angelo 4 amenewa anali ndi mapiko 6 ndipo mapikowo anali ndi maso paliponse.+ Angelo amenewa sankapuma masana ndi usiku, ankangokhalira kunena kuti: “Woyera, woyera, woyera ndi Yehova*+ Mulungu, Wamphamvuyonse, amene analipo, amene alipo ndi amene akubwera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena