Danieli 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mtima wake usinthidwe kuchoka kumtima wa munthu nʼkukhala mtima wa nyama ndipo padutse+ nthawi zokwana 7.+
16 Mtima wake usinthidwe kuchoka kumtima wa munthu nʼkukhala mtima wa nyama ndipo padutse+ nthawi zokwana 7.+