-
Danieli 4:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Alonda ndi amene alamula zimenezi.+ Amithenga oyera ndi amene apempha zimenezi nʼcholinga chakuti anthu adziwe kuti Mulungu Wamʼmwambamwamba ndi Wolamulira wa maufumu a anthu,+ ndiponso adziwe kuti iye amapereka ulamuliro kwa aliyense amene akufuna kumupatsa ndipo amaika ngakhale munthu wonyozeka kwambiri kuti azilamulira.”
-