-
Danieli 5:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Anachita zimenezi chifukwa Danieli, amene mfumu inamupatsa dzina lakuti Belitesazara,+ anali ndi luso lodabwitsa, anali wodziwa zinthu ndi wozindikira pa nkhani yomasulira maloto, kumasulira mikuluwiko komanso kuthana ndi zinthu zovuta.*+ Tsopano itanani Danieli ndipo akuuzani kumasulira kwa mawu amenewa.”
-