Danieli 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense amene sagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi nʼkulambira fanolo, nthawi yomweyo aponyedwa mungʼanjo yoyaka moto.”+
6 Aliyense amene sagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi nʼkulambira fanolo, nthawi yomweyo aponyedwa mungʼanjo yoyaka moto.”+