Danieli 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mfumu inalamula Asipenazi, mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu kuti abweretse ena mwa Aisiraeli,* kuphatikizapo a mʼbanja lachifumu komanso anthu olemekezeka.+ Danieli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pagulu la anyamatawo panali anyamata ena a fuko la Yuda.* Mayina awo anali Danieli,*+ Hananiya,* Misayeli* ndi Azariya.*+ Danieli 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mofulumira, Arioki anapititsa Danieli kwa mfumu nʼkuiuza kuti: “Ndapeza munthu pakati pa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda+ yemwe angamasulire maloto anu mfumu.” Danieli 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anabweretsa Danieli kwa mfumu ndipo mfumuyo inamufunsa kuti: “Kodi iwe ndiwe Danieli, mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda ndi bambo anga mfumu?+
3 Ndiyeno mfumu inalamula Asipenazi, mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu kuti abweretse ena mwa Aisiraeli,* kuphatikizapo a mʼbanja lachifumu komanso anthu olemekezeka.+
6 Pagulu la anyamatawo panali anyamata ena a fuko la Yuda.* Mayina awo anali Danieli,*+ Hananiya,* Misayeli* ndi Azariya.*+
25 Mofulumira, Arioki anapititsa Danieli kwa mfumu nʼkuiuza kuti: “Ndapeza munthu pakati pa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda+ yemwe angamasulire maloto anu mfumu.”
13 Choncho anabweretsa Danieli kwa mfumu ndipo mfumuyo inamufunsa kuti: “Kodi iwe ndiwe Danieli, mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda ndi bambo anga mfumu?+