Esitere 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiye inu lembani makalata mʼmalo mwa Ayuda. Mulembe mʼdzina la mfumu zilizonse zimene mukuona kuti nʼzabwino ndipo mudinde makalatawo ndi mphete yodindira ya mfumu. Chifukwa nʼzosatheka kufafaniza lamulo limene lalembedwa mʼdzina la mfumu nʼkudindidwa ndi mphete yake yodindira.”+ Danieli 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno inu mfumu khazikitsani lamulo ndipo musaine+ kuti lamulolo lisasinthe, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya, amene sangasinthidwe.”+
8 Ndiye inu lembani makalata mʼmalo mwa Ayuda. Mulembe mʼdzina la mfumu zilizonse zimene mukuona kuti nʼzabwino ndipo mudinde makalatawo ndi mphete yodindira ya mfumu. Chifukwa nʼzosatheka kufafaniza lamulo limene lalembedwa mʼdzina la mfumu nʼkudindidwa ndi mphete yake yodindira.”+
8 Ndiyeno inu mfumu khazikitsani lamulo ndipo musaine+ kuti lamulolo lisasinthe, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya, amene sangasinthidwe.”+