Danieli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imene Belisazara+ anali mfumu anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu ndipo iyeyo ankamwa vinyo atakhala patsogolo pawo.+ Danieli 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa.+
5 Pa nthawi imene Belisazara+ anali mfumu anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu ndipo iyeyo ankamwa vinyo atakhala patsogolo pawo.+