Salimo 104:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 104 Moyo wanga utamande Yehova.+ Inu Yehova Mulungu wanga, ndinu wamkulu kwambiri.+ Mwavala ulemu ndi ulemerero.+ 2 Mwadzifunditsa kuwala+ ngati chofunda,Mwatambasula kumwamba ngati nsalu yopangira tenti.+
104 Moyo wanga utamande Yehova.+ Inu Yehova Mulungu wanga, ndinu wamkulu kwambiri.+ Mwavala ulemu ndi ulemerero.+ 2 Mwadzifunditsa kuwala+ ngati chofunda,Mwatambasula kumwamba ngati nsalu yopangira tenti.+