Danieli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma oyera a Mulungu Wamkulu+ adzalandira ufumu+ ndipo ufumuwo udzakhala wawo+ mpaka kalekale, inde kwamuyaya.’ Danieli 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ufumu, ulamuliro, ndi ulemerero wa maufumu apadziko lonse lapansi zinaperekedwa kwa anthu amene ndi oyera a Mulungu Wamkulu.+ Ufumu wawo udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo maulamuliro onse adzawatumikira ndi kuwamvera.’
18 Koma oyera a Mulungu Wamkulu+ adzalandira ufumu+ ndipo ufumuwo udzakhala wawo+ mpaka kalekale, inde kwamuyaya.’
27 Ufumu, ulamuliro, ndi ulemerero wa maufumu apadziko lonse lapansi zinaperekedwa kwa anthu amene ndi oyera a Mulungu Wamkulu.+ Ufumu wawo udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo maulamuliro onse adzawatumikira ndi kuwamvera.’