-
Danieli 7:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mtsinje wa moto unkayenda kuchokera kwa iye.+ Panali atumiki okwana 1 miliyoni* amene ankatumikira nthawi zonse ndi atumiki enanso 100 miliyoni* amene ankatumikira pamaso pake nthawi zonse.+ Bwalo la milandu+ linayamba kuzenga mlandu ndipo mabuku anatsegulidwa.
11 Pa nthawi imeneyo, ndinapitirizabe kuyangʼana chifukwa ndinkamva mawu odzitukumula* amene nyanga ija inkalankhula.+ Ndinapitiriza kuyangʼana mpaka pamene chilombocho chinaphedwa ndipo thupi lake linaponyedwa pamoto nʼkuwonongedwa.
-