Danieli 5:30, 31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa.+ 31 Dariyo+ Mmedi anapatsidwa ufumuwo ndipo anali ndi zaka pafupifupi 62.
30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa.+ 31 Dariyo+ Mmedi anapatsidwa ufumuwo ndipo anali ndi zaka pafupifupi 62.