-
Ezara 8:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Kenako ndinalamula kuti tisale kudya tili kumtsinje wa Ahava komweko, kuti tidzichepetse pamaso pa Mulungu wathu nʼkumupempha kuti atitsogolere pa ulendo wathu, pamodzi ndi ana athu ndi katundu wathu yense.
-