Nehemiya 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma iwo anali osamvera ndipo anakugalukirani.+ Anasiya kutsatira Chilamulo chanu, anapha aneneri anu amene ankawachenjeza kuti abwerere kwa inu ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+
26 Koma iwo anali osamvera ndipo anakugalukirani.+ Anasiya kutsatira Chilamulo chanu, anapha aneneri anu amene ankawachenjeza kuti abwerere kwa inu ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+