Maliro 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova wachita zimene ankafuna.+ Wakwaniritsa zimene ananena,+Zimene analamula kalekale.+ Wakuwononga mopanda chisoni.+ Wachititsa kuti adani ako asangalale chifukwa cha zimene zakuchitikira. Wawonjezera mphamvu* za adani ako.
17 Yehova wachita zimene ankafuna.+ Wakwaniritsa zimene ananena,+Zimene analamula kalekale.+ Wakuwononga mopanda chisoni.+ Wachititsa kuti adani ako asangalale chifukwa cha zimene zakuchitikira. Wawonjezera mphamvu* za adani ako.