Salimo 89:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukamalamulira, nthawi zonse mumachita zinthu mwachilungamo komanso molungama.+Nthawi zonse mumasonyeza kukhulupirika komanso chikondi chokhulupirika.+ Yesaya 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usiku ndimakulakalakani ndi mtima wanga wonse,Inde, ndimakufunafunani ndi mtima wonse.+Chifukwa mukaweruza dziko lapansi,Anthu okhala mʼdzikoli amaphunzira zokhudza chilungamo.+
14 Mukamalamulira, nthawi zonse mumachita zinthu mwachilungamo komanso molungama.+Nthawi zonse mumasonyeza kukhulupirika komanso chikondi chokhulupirika.+
9 Usiku ndimakulakalakani ndi mtima wanga wonse,Inde, ndimakufunafunani ndi mtima wonse.+Chifukwa mukaweruza dziko lapansi,Anthu okhala mʼdzikoli amaphunzira zokhudza chilungamo.+