Yeremiya 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Mundiitane ndipo ndidzakuyankhani. Nthawi yomweyo ndidzakuuzani zinthu zazikulu ndi zovuta kuzimvetsa zimene simukuzidziwa.’”+ 1 Akorinto 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu anatiululira ifeyo zinthu zimenezi+ kudzera mwa mzimu wake,+ chifukwa mzimu umafufuza zinthu zonse, ngakhale zinthu zozama za Mulungu.+
3 ‘Mundiitane ndipo ndidzakuyankhani. Nthawi yomweyo ndidzakuuzani zinthu zazikulu ndi zovuta kuzimvetsa zimene simukuzidziwa.’”+
10 Mulungu anatiululira ifeyo zinthu zimenezi+ kudzera mwa mzimu wake,+ chifukwa mzimu umafufuza zinthu zonse, ngakhale zinthu zozama za Mulungu.+