Numeri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Uza Aroni ndi ana ake kuti, ‘Mukamadalitsa+ Aisiraeli muziwauza kuti: Numeri 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova asonyeze kuti akusangalala nanu+ ndipo akukomereni mtima.