1 Mafumu 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mumve pemphero lopempha chifundo la mtumiki wanu komanso la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayangʼana malo ano. Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ mumve nʼkukhululuka.+
30 Mumve pemphero lopempha chifundo la mtumiki wanu komanso la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayangʼana malo ano. Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ mumve nʼkukhululuka.+