Danieli 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako iye anandiuza kuti: “Iwe Danieli, munthu wokondedwa* kwambiri,+ mvetsera mwatcheru mawu amene ndikufuna kukuuza. Tsopano imirira chifukwa ine ndatumidwa kwa iwe.” Atandiuza zimenezi, ndinaimirira koma ndikunjenjemera. Danieli 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anandiuza kuti: “Iwe munthu wokondedwa kwambiri,*+ usachite mantha.+ Mtendere ukhale nawe.+ Limba mtima, ndithu limba mtima.” Akulankhula nane, ndinalimbikitsidwa ndipo ndinanena kuti: “Lankhulani mbuyanga chifukwa inu mwandilimbikitsa.”
11 Kenako iye anandiuza kuti: “Iwe Danieli, munthu wokondedwa* kwambiri,+ mvetsera mwatcheru mawu amene ndikufuna kukuuza. Tsopano imirira chifukwa ine ndatumidwa kwa iwe.” Atandiuza zimenezi, ndinaimirira koma ndikunjenjemera.
19 Kenako anandiuza kuti: “Iwe munthu wokondedwa kwambiri,*+ usachite mantha.+ Mtendere ukhale nawe.+ Limba mtima, ndithu limba mtima.” Akulankhula nane, ndinalimbikitsidwa ndipo ndinanena kuti: “Lankhulani mbuyanga chifukwa inu mwandilimbikitsa.”