Salimo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,Ndipo anthu olemekezeka asonkhana pamodzi* mogwirizana+Kuti alimbane ndi Yehova komanso wodzozedwa wake.*+ Yohane 1:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choyamba iyeyu anakumana ndi mchimwene wake Simoni ndipo anamuuza kuti: “Ifetu tapeza Mesiya”+ (dzina limeneli akalimasulira limatanthauza, “Khristu”),
2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,Ndipo anthu olemekezeka asonkhana pamodzi* mogwirizana+Kuti alimbane ndi Yehova komanso wodzozedwa wake.*+
41 Choyamba iyeyu anakumana ndi mchimwene wake Simoni ndipo anamuuza kuti: “Ifetu tapeza Mesiya”+ (dzina limeneli akalimasulira limatanthauza, “Khristu”),