7 Mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu anapatsa anyamatawa mayina ena. Danieli anamupatsa dzina lakuti Belitesazara,+ Hananiya anamupatsa dzina lakuti Shadireki, Misayeli anamupatsa dzina lakuti Misheki ndipo Azariya anamupatsa dzina lakuti Abedinego.+