Salimo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Mitundu ya anthu yawonongedwa, yachotsedwa padziko lapansi.+ Salimo 90:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mapiri asanabadwe,Kapena musanakhazikitse dziko lapansi komanso nthaka,+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+ Yeremiya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake.
2 Mapiri asanabadwe,Kapena musanakhazikitse dziko lapansi komanso nthaka,+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+
10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake.