Danieli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nkhani iliyonse yofunika nzeru komanso kuzindikira, imene mfumu inkawafunsa, inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake wonse. Danieli 2:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kenako mfumu inamukweza pa udindo Danieli ndipo inamupatsa mphatso zambiri zabwino. Inamuikanso kuti akhale wolamulira wa chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso mkulu wa akuluakulu a boma amene ankayangʼanira amuna onse anzeru a mʼBabulo.
20 Pa nkhani iliyonse yofunika nzeru komanso kuzindikira, imene mfumu inkawafunsa, inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake wonse.
48 Kenako mfumu inamukweza pa udindo Danieli ndipo inamupatsa mphatso zambiri zabwino. Inamuikanso kuti akhale wolamulira wa chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso mkulu wa akuluakulu a boma amene ankayangʼanira amuna onse anzeru a mʼBabulo.