Danieli 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma chifukwa ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo ndi mizu yake,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndi amene akulamulira kumwamba.
26 Koma chifukwa ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo ndi mizu yake,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndi amene akulamulira kumwamba.